Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Timoteo 4:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Ambuye anaima nane nandipatsa mphamvu; kuti mwa ine cilalikiro cimveke konse konse, ndi amitundu onse amve; ndipo ndinalanditsidwa m'kamwa mwa mkango.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 4

Onani 2 Timoteo 4:17 nkhani