Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Timoteo 2:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma m'nyumba yaikuru simuli zotengera za golidi ndi siliva zokha, komatunso za mtengo ndi dothi; ndipo zina zaulemu, koma zina zopanda ulemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 2

Onani 2 Timoteo 2:20 nkhani