Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Atesalonika 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amene atsutsana nazo, nadzikuza pa zonse zochedwa Mulungu, kapena zopembedzeka; kotero kuti iye wakhalapansi ku Kacisi wa Mulungu, nadzionetsera yekha kuti ali Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 2 Atesalonika 2

Onani 2 Atesalonika 2:4 nkhani