Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Atesalonika 2:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti musamagwedezeka mtima msanga ndi kutaya maganizo anu, kapena kuopsedwa, mwa mzimu kapena mwa mau; kapena mwa kalata, monga wolembedwa ndi ife, monga ngati tsiku la Ambuye lafika;

Werengani mutu wathunthu 2 Atesalonika 2

Onani 2 Atesalonika 2:2 nkhani