Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 6:16-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Ndipo ciphatikizo cace ncanji ndi kacisi wa Mulungu ndi wa mafano? Pakuti ife ndife kacisi wa, Mulungu wamoyo; monga Mulungu anati, Ndidzakhalitsa mwa iwo, ndipe ndidzayendayenda mwa iwo; ndipo ndidzakhala Mulungu wao, ndi iwo adzakhala anthu anga.

17. Cifukwa cace,Turukani pakati Pao, ndipo patukani, ati Ambuye,Ndipo musakhudza kanthu kosakonzeka;Ndipo Ine ndidzalandira inu,

18. Ndipo ndidzakhala kwa inu Atate,Ndi inu mudzakhala kwa Ine ana amunandi akazi,anena Ambuye Wamphamvuyonse.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 6