Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 6:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ciphatikizo cace ncanji ndi kacisi wa Mulungu ndi wa mafano? Pakuti ife ndife kacisi wa, Mulungu wamoyo; monga Mulungu anati, Ndidzakhalitsa mwa iwo, ndipe ndidzayendayenda mwa iwo; ndipo ndidzakhala Mulungu wao, ndi iwo adzakhala anthu anga.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 6

Onani 2 Akorinto 6:16 nkhani