Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti tidziwa kuti ngati nyumba ya pansi pano ya msasa wathu ipasuka, tiri naco cimango ca kwa Mulungu, ndiyo nyumba yosamangidwa ndi manja, yosatha, m'Mwamba.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 5

Onani 2 Akorinto 5:1 nkhani