Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 3:8-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. koposa kotani nanga utumiki wa Mzimu udzakhala m'ulemerero?

9. Pakuti ngati utumiki wa citsutso unali wa ulemerero, makamaka utumiki wa cilungamo ucurukira muulemerero kwambiri.

10. Pakutinso cimene cinacitidwa ca ulemerero sicinacitidwa ca ulemerero m'menemo, cifukwa ca ulemerero woposawo.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 3