Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komangati utumiki wa imfa wolembedwa ndi wolocedwa m'miyala, unakhala m'ulemerero, kotero kuti ana a Israyeli sanathe kuyang'anitsa pankhope yace ya Mose, cifukwa ca ulemerero wa nkhope yace, umene unalikucotsedwa:

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 3

Onani 2 Akorinto 3:7 nkhani