Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 3:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma mitima yao inaumitsidwa; pakuti kufikira lero lomwe lino, pa lcuwerenga kwa pangano lakale cophimba comweci cikhalabe cosabvundukuka, cimene cirikucotsedwa mwa Kristu.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 3

Onani 2 Akorinto 3:14 nkhani