Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 12:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena kwa ine, Cisomo canga cikukwanira; pakuti mphamvu yanga ithedwa m'ufoko. Cifukwa cace makamaka ndidzadzitamandira rriokondweratu m'maufoko anga, kuti mphamvu ya Kristu ikhale pa ine.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 12

Onani 2 Akorinto 12:9 nkhani