Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 1:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati tisautsidwa, kuli cifukwa ca citonthozo ndi cipulumutso canu; ngati titonthozedwa, kuli kwa citonthozo canu cimene cicititsa mwa kupirira kwa masautso omwewo amene ifenso timva.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 1

Onani 2 Akorinto 1:6 nkhani