Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 2:28-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

28. Ndipo tsopano, tiana, khalani mwa iye; kuti 10 akaonekere iye tikakhale nako kulimbika mtima, osacita manyazi kwa iye pa kudza kwace.

29. Ngati mudziwa kuti ali wolungama, muzindikira kuti 11 ali yensenso wakucita cilungamo abadwa kucokera mwa iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 2