Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 2:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo inu, 8 kudzoza kumene munalandira kucokera kwa iye, kukhala mwa inu, ndipo simusowa kuti wina akuphunzitseni; koma 9 monga kudzoza kwace kukuphunzitsani za zinthu zonse, ndipo kuli koona, sikuli bodza ai, ndipo monga kudaphunzitsa inu, mukhale mwa iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 2

Onani 1 Yohane 2:27 nkhani