Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 2:24-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Koma inu, cimene munacimva kuyambira paciyambi cikhale mwa Inu, 6 Ngari cikhala mwa inu cimene mudacimva kuyambira paciyambi, inunso mudzakhalabe mwa Mwana, ndi mwa Atate.

25. Ndipo 7 ili ndi lonjezano iye anatiloniezera ife, ndiwo moyo wosatha.

26. Izi ndakulemberani za iwo akusokeretsa inu.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 2