Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Yohane 1:8-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Tikati kuti tiribe ucimo, tidzinyenga tokha, ndipo mwa ife mulibe coonadi.

9. Ngati tibvomereza macimo athu, ali wokhulupirika ndi wolungama iye, kuti atikhululukire macimo athu, ndi kutisambitsa kuticotsera cosalungama ciri conse.

10. Tikanena kutisitidacimwa, timuyesa iye wonama, ndipo mau ace sakhala mwa ife.

Werengani mutu wathunthu 1 Yohane 1