CIMENE cinaliko kuyambira paciyambi, cimene tidacimva, cimene tidaciona m'maso mwathu, cimene tidacipenyerera, ndipo manja athu adacigwira ca Mau a moyo,