Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Atesalonika 5:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ife popeza tiri a usana tisaledzere, titabvala capacifuwa ca cikhulupiriro ndi cikondi; ndi cisoti ciri ciyembekezo ca cipulumutso.

Werengani mutu wathunthu 1 Atesalonika 5

Onani 1 Atesalonika 5:8 nkhani