Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Atesalonika 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kukumbukila kosalekeza nchito yanu ya cikhulupiriro, ndi cikondi cocitacita, ndi cipiriro ca ciyembekezo ca Ambuye wathu Yesu Kristu, pamaso pa Mulungu Atate wathu;

Werengani mutu wathunthu 1 Atesalonika 1

Onani 1 Atesalonika 1:3 nkhani