Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 7:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mkazi alibe ulamuliro wa pa thupi lace la iye yekha, koma mwamuna ndiye; koma momwemonso mwamuna alibe ulamuliro wa pa thupi laiye yekha, koma mkazi ndiye.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7

Onani 1 Akorinto 7:4 nkhani