Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 7:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti iye amene anaitanidwa mwa Ambuye, pokhala ali kapolo, ali mfulu ya Ambuye: momwemonso woitanidwayo, pokhala ali mfulu, ali kapolo wa Kristu.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7

Onani 1 Akorinto 7:22 nkhani