Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 7:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma za izi munalembazi; kuli bwino kwa munthu kusakhudza mkazi.

2. Koma cifukwa ca madama munthu yense akhale naye mkazi wa iye yekha, ndi mkazi yense akhale naye mwamuna wa iye yekha.

3. Mwamunayo apereke kwa mkazi mangawa ace; koma modzimodzinso mkazi kwa mwamuna.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7