Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 5:12-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Pakuti nditani nao akunja kukaweruza iwo? Kodi amene ali m'katimosimuwaweruza ndi inu,

13. komaakunia awaweruza Mulungu? Cotsani woipayo pakati pa inu nokha.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 5