Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 5:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma tsopano ndalembera inu kuti musayanjane naye, ngati wina wochedwa mbale ali wacigololo, kapena wosirira, kapena wopembedza mafano, kapena wolalatira, kapena woledzera, kapena wolanda, kungakhale kukadya naye wotere, iai.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 5

Onani 1 Akorinto 5:11 nkhani