Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 4:18-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Koma ena adzitukumula, monga ngati sindinalinkudza kwa inu.

19. Koma ndidzafika kwa inu msanga, akandilola Ambuye; ndipo ndidzazindikira si mau a iwo odzitukumula, koma mphamvuyi.

20. Pakuti ufumu wa Mulungu suli m'mau, koma mumphamvu, Mufuna ciani?

21. Kodi ndifike kwa inu ndi ndodo, kapena mwacikondi, ndi mzimu wakufatsa?

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 4