Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 4:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa ca ici ndatuma kwa inu Timoteo, ndiye mwana wanga wokondedwa ndi wokhulupirika mwa Ambuye, amene adzakumbutsa inu njira zanga za mwa Kristu, monga ndiphunzitsa ponsepom'Mipingo yonse.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 4

Onani 1 Akorinto 4:17 nkhani