Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 8:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu: Alimbike manja anu, inu akumva masiku ano mau awa pakamwa pa aneneri amene anakhalako tsiku lakuikidwa maziko a nyumba ya Yehova wa makamu, ndiyo Kacisi, kuti amangidwe.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 8

Onani Zekariya 8:9 nkhani