Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 6:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo akukhala kutari adzafika, nadzamanga ku Kacisi wa Yehova, ndipo inu mudzadziwa kuti Yehova wa makamu ananditumiza kwa inu. Ndipo ici cidzacitika ngati mudzamvera mwacangu mau a Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 6

Onani Zekariya 6:15 nkhani