Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 5:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinakweza maso anga, ndinapenya, ndipo taonani, anaturuka akazi awiri, ndi m'mapiko mwao munali mphepo; ndipo anali nao mapiko ngati mapiko a cumba, nanyamula efayo pakati pa dziko ndi thambo.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 5

Onani Zekariya 5:9 nkhani