Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 14:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mudzathawa kudzera cigwa ca mapiri anga; pakuti cigwa ca mapiri cidzafikira ku Azali; ndipo mudzathawa monga umo munathawira cibvomezi, masiku a Uziya mfumu ya Yuda; ndipo Yehova Mulungu wanga adzadza, ndi opatulika onse pamodzi ndi Inu.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 14

Onani Zekariya 14:5 nkhani