Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 14:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndidzasonkhanitsa amitundu onse alimbane ndi Yerusalemu; ndipo mudziwo udzalandidwa, ndi nyumba zidzafunkhidwa, ndi akazi adzakakamizidwa; ndi limodzi la magawo awiri la mudzi lidzaturuka kumka kundende, koma anthu otsala sadzaonongeka m'mudzimo.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 14

Onani Zekariya 14:2 nkhani