Ndipo kudzali tsiku lomwelo, kuti cisokonezo cacikuru cocokera kwa Yehova cidzakhala pakati pao; ndipo adzagwira yense dzanja la mnzace; ndi dzanja lace lidzaukira dzanja la mnzace.