Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 14:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mliri umene Yehova adzakantha nao mitundu yonse ya anthu imene idathira nkhondo pa Yerusalemu ndi uwu: nyama yao idzaonda akali ciriri pa mapazi ao, ndi maso ao adzapuala m'pfunkha mwao, ndi lilime lao lidzanyala m'kamwa mwao.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 14

Onani Zekariya 14:12 nkhani