Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 12:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku ilo ndidzaika akalonga a Yuda ngati phale la moto pansi pa nkhuni, ndi ngati muuni wamoto mwa mitolo ya tirigu; ndipo adzatha mitundu yonse ya anthu pozungulirapo, ku dzanja lamanja ndi lamanzere; ndipo Yerusalemu adzakhalanso m'malo mwace, m'Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 12

Onani Zekariya 12:6 nkhani