Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 12:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ndidzaika Yerusalemu akhale cipanda codzandiritsa kwa mitundu yonse ya anthu yozungulirapo, ndipo cidzafikira Yuda yemwe pomangira misasa Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 12

Onani Zekariya 12:2 nkhani