Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zekariya 11:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

zimene eni ace azipha, nadziyesera osaparamula; ndi iwo akuwagulitsa akuti, Alemekezedwe Yehova, pakuti ine ndine wolemera; ndi abusa ao sazicitira cifundo.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 11

Onani Zekariya 11:5 nkhani