Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Zefaniya 1:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

MAU a Yehova amene anadza kwa Zefaniya mwana wa Kusi, mwana wa Gedaliya, mwana wa Amariya, mwana wa Hezekiya, masiku a Yosiya, mwana wa Amoni mfumu ya Yuda.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 1

Onani Zefaniya 1:1 nkhani