Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 8:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

monga Mose mtumiki wa Mulungu adalamulira ana a Israyeli, monga mulembedwa m'buku la cilamulo ca Mose, guwa la nsembe la miyala yosasema, yoti palibe munthu anakwezapo citsulo; ndipo anafukizirapo Yehova nsembe zopsereza, naphera nsembe zoyamika.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:31 nkhani