Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 8:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

A kumudzinso anawaturukira; potero anakhala pakati pa Israyeli, ena mbali yina, ena mbali yina; ndipo anawakantha, mpaka sanatsala kapena kupulumuka wa iwo ndi mmodzi yense.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:22 nkhani