Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 8:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakupenya Yoswa ndi Israyeli yense kuti olalirawo adagwira mudzi, ndi kuti utsi wa mudzi unakwera, anabwerera, nawapha amuna a ku Ai.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:21 nkhani