Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 8:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo uzimcitira Ai ndi mfumu yace monga umo unamcitira Yeriko ndi mfumu yace; koma zofunkha zace ndi ng'ombe zace mudzifunkhire nokha; udziikire anthu aja lire kukhonde kwa mudzi.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:2 nkhani