Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 6:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atanena kwa anthu Yoswa, ansembe asanu ndi awiri akunyamula mphalasa zisanu ndi ziwiri zanyanga za nkhosa zamphongo pamaso pa Yehova, anapita naliza mphalasazo; ndipo likasa la cipangano ca Yehova linawatsata.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 6

Onani Yoswa 6:8 nkhani