Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 6:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ansembe asanu ndi awiri azinyamula mphalasa zisanu ndi ziwiri zanyanga: za nkhosa zamphongo, natsogolere nazo likasa; koma tsiku lacisanu ndi ciwiri muzizungulira mudziwo kasanu ndi kawirio ndi ansembe aziliza mphalasazo.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 6

Onani Yoswa 6:4 nkhani