Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 6:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anawalumbirira nyengo ija, ndi kuti, Wotembereredwa pamaso pa Yehova munthu amene adzauka ndi kumanga mudzi uwu wa Yeriko; adzamanga kuzika kwace ndi kutayapo mwana wace woyamba, nadzaimika zitseko zace ndi kutayapo mwana wace wotsirizira.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 6

Onani Yoswa 6:26 nkhani