Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 6:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Rahabi, mkazi wadamayo ndi banja la atate wace, ndi onse anali nao, Yoswa anawasunga ndi moyo; ndipo anakhala pakati pa Israyeli mpaka lero tino; cifukwa anabisa mithenga imene Yoswa anaituma kuzonda Yeriko.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 6

Onani Yoswa 6:25 nkhani