Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 23:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukalakwira cipangano ca Yehova Mulungu wanu cimene analamulira inu ndi kumuka ndi kutumikira milungu yina ndi kuigwadira, mkwiyo wa Mulungu udzayakira inu, nimudzatayika msanga m'dziko lokomali anakupatsani.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 23

Onani Yoswa 23:16 nkhani