Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 22:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma samalirani bwino kuti mucite cilangizo ndi cilamulo zimene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani kukonda Yehova Mulungu wanu, ndi kuyenda m'njira zace zonse ndi kusunga malamulo ace, ndi kumuumirira iye, ndi kumtumikira iye ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 22

Onani Yoswa 22:5 nkhani