Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 22:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi Akani mwana wa Zera sanalakwa m'coperekedwaco, ndipo mkwiyo unagwera msonkhano wonse wa Israyeli? osangoonongeka yekha munthuyo mu mphulupulu yace.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 22

Onani Yoswa 22:20 nkhani