Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 22:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mukayesa dziko La colowa canu ncodetsa, olokani kulowa m'dziko lacolowaca Yehova m'mene cihemaca Yehovacikhalamo, nimukhale naco colowa pakati pa ife; koma musapikisana ndi Yehova kapena kupikisana nafe, ndi kudzimangira nokha guwa la nsembe, pamodzi ndi guwa la nsembe la Yehova Mulungu wathu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 22

Onani Yoswa 22:19 nkhani