Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 20:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapatula Kedesi m'Galileya ku mapiri a Nafitali, ndi Sekemu ku mapiri a Efraimu, ndi mudzi wa Ariba ndiwo Hebroni ku mapiri a Yuda.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 20

Onani Yoswa 20:7 nkhani